1201

SERMON TOPIC: MAZIKO OKHAZIKIKA- 6 - CHIWERUZO CHA MUYAYA

Speaker: David Makiyi

Language: CHICHEWA

Date: 5 June 2013

Topic Groups: 1ST PRINCIPLES

Sermon synopsis: Aroma 2:5-11
Koma kolingana ndikuuma kwako,ndimtima wako osalapa, ulikudziunjikira wekha mkwiyo padzuwa la mkwiyo ndi la kubvumbulutsa kuweruza, adzabwezera munthu aliyense kolingana ndi ntchito zache; kwa iwo amene anafunafuna ulemerero ndi ulemu ndichisaonongeko, mwakupilira pantchito zabwino adzabwezera moyo osatha; koma kwa iwo andeu, ndi osamvera choonadi,koma amvera chosalungama, adzabwezera mkwiyo ndi kuzaza,nsautso ndikuwawa mtima, kwa moyo wa munthu aliyense wakuchita zoipa kuyambira Myuda,komanso Mhelene; pakuti Mulungu alibe tsankhu.
- Download notes (39 KB, 6364 downloads)

- Download audio (7.61 MB, 3757 downloads)
- All sermons by David Makiyi

- All sermons on 1ST PRINCIPLES

- All sermons in CHICHEWA




IP:Country:City:Region: